Kusiyana pa kagwilidwe ka ntchito pakati pa amayi ndi abambo ndikuphwanya ufulu wachibadwidwe kwakukulu lero. Kukonza vuto limene lakhudza dziko lonse lapansili, ndi kukwanilitsa kusasiyana pakagwilidwe ka ntchito pakati pa amayi ndi abambo, ndikofunikira kuti abambo ndi anyamata atenge nawo mbali pokambilana ndikukhala nawo mbali yosintha zinthu.
Kusonkhanitsa abambo ndi anyamata kuti pasakhale Kusiyana pa kagwilidwe ka ntchito pakati pa amayi ndi abambo
Powered by BetterDocs